Friday, May 3, 2024
HomeVideoCAUSE OF DEATH: Ochita zisudzo odziwika bwino wamdziko la Nigeria, John Okafor,...

CAUSE OF DEATH: Ochita zisudzo odziwika bwino wamdziko la Nigeria, John Okafor, kapena kuti Mr Ibu, wamwalira


Ochita zisudzo odziwika bwino wamdziko la Nigeria John Okafor kapena kuti Mr Ibu, wamwalira.


Mr Ibu akhala akudwala kwa pakanthawi, ndipo amwalira lero mumzinda wa Lagos kwawo ku Nigeria. 

Mr Ibu ndiwo adadziwika kwambiri mzaka zama 2000, ndipo filimu yoti Mr Ibu anayijambula mu 2004 ndi ana ozunguza omwe amadziwika kuti Aki and Pawpaw mu filimumo.

Kalelo munthu ukamaonera filimu yoti muli Mr Ibu, nanjinanji mukhaleso tiana tosautsato, munthu umadziwilatu kuti apa ting’amba mapapo ndikuseka.

READ ALSO  PHOTO: GOP fans react as Donald Trump interview with Tucker Carlson on X hit 200 MILLION views

WATCH VIDEO

DOWNLOAD VIDEO

RELATED ARTICLES
- Advertisment -

Most Popular

- Advertisment -
- Advertisment -